Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 14
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la Chivumbulutso

      • Mwanawankhosa ndi enanso 144,000 (1-5)

      • Mauthenga ochokera kwa angelo atatu (6-12)

        • Mngelo amene ali ndi uthenga wabwino, akuuluka mumlengalenga (6, 7)

      • Osangalala ndi anthu amene akufa ali ogwirizana ndi Khritsu (13)

      • Anakolola mpesa kawiri padziko lapansi (14-20)

Chivumbulutso 14:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 1:29; Chv 5:6; 22:3
  • +Sl 2:6; Ahe 12:22; 1Pe 2:6
  • +Chv 7:4
  • +Chv 3:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 31

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2006, tsa. 5

    7/1/1995, tsa. 13

    12/15/1988, tsa. 20

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 198-200

Chivumbulutso 14:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 200

Chivumbulutso 14:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 33:3; 98:1; 149:1; Chv 5:9
  • +Chv 4:6
  • +Chv 4:4; 19:4
  • +Chv 7:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 31

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 200-201, 202-203

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, tsa. 20

Chivumbulutso 14:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 11:2; Yak 1:27; 4:4
  • +1Pe 2:21
  • +1Ak 6:20; 7:23; Chv 5:9
  • +Yak 1:18

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 24

    1/1/2007, tsa. 22

    2/15/2006, ptsa. 19-20

    6/1/1989, ptsa. 12-13

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 201-203

Chivumbulutso 14:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aef 5:25-27; Yuda 24

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 24

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 201-202

Chivumbulutso 14:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 24:14; Mko 13:10; Mac 1:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    7/2022, tsa. 9

    5/2022, ptsa. 6-7

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 5

    Nsanja ya Olonda,

    1/1/2007, tsa. 19

    12/15/2004, ptsa. 18-19

    12/1/1999, ptsa. 9-11

    11/1/1995, tsa. 8

    6/15/1992, ptsa. 14-15

    1/1/1990, tsa. 3

    12/15/1988, tsa. 20

    1/1/1988, tsa. 16

    5/15/1987, ptsa. 12-13

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 203-205, 313

    Mphunzitsi Waluso, tsa. 65

Chivumbulutso 14:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Pe 2:9
  • +Eks 20:11; Sl 146:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/1/2007, tsa. 19

    10/1/2005, ptsa. 23-25

    12/1/1999, ptsa. 10-11

    6/15/1998, tsa. 20

    1/1/1990, ptsa. 14-15

    1/1/1989, ptsa. 29-30

    12/15/1988, ptsa. 19-24

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 203-205

    Dikirani!, ptsa. 12-14

    Mphunzitsi Waluso, tsa. 65

    Sukulu ya Utumiki, ptsa. 272-275

Chivumbulutso 14:8

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “imwe mkwiyo wa.”

  • *

    MʼChigiriki por·nei′a. Onani Matanthauzo a Mawu Ena.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 17:18
  • +Yes 21:9; Chv 18:21
  • +Yer 51:7, 8; Chv 17:1, 2; 18:2, 3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 205-209, 245

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/2005, tsa. 24

    5/1/1989, ptsa. 3-5

    4/15/1989, ptsa. 4-9

    4/1/1989, tsa. 21

    12/15/1988, ptsa. 20-21

    1/1/1988, tsa. 16

    Yesaya 1, ptsa. 223-224

Chivumbulutso 14:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 13:1
  • +Chv 13:15, 16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 209-210

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/2005, ptsa. 24-25

    1/1/1988, tsa. 16

Chivumbulutso 14:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 75:8; Chv 11:18; 16:19
  • +Chv 21:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 209-211

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/1993, tsa. 7

    Kukambitsirana, ptsa. 147-148

Chivumbulutso 14:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 25:46; 2At 1:9; Chv 19:3
  • +Chv 13:16-18; 16:2; 20:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 210-211

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/1993, tsa. 7

    Kukambitsirana, ptsa. 147-148

Chivumbulutso 14:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ahe 10:38
  • +Chv 13:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 210-211

Chivumbulutso 14:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 15:51, 52; 1At 4:16, 17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 211

Chivumbulutso 14:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 7:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 88-89

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/2010, ptsa. 26-27

    12/15/1988, tsa. 21

    1/1/1988, tsa. 11

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 211

Chivumbulutso 14:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 13:30

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 88-89

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/2010, ptsa. 26-27

    1/1/1988, tsa. 11

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 211-212

Chivumbulutso 14:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, tsa. 88

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/2010, ptsa. 26-27

    12/15/1988, tsa. 21

    1/1/1988, tsa. 11

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 211-212

Chivumbulutso 14:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 212

Chivumbulutso 14:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yow 3:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 4

    6/1/1999, ptsa. 6-7

    1/1/1988, tsa. 18

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 212

Chivumbulutso 14:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 19:11, 15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 212-213, 215

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, tsa. 21

Chivumbulutso 14:20

Mawu a M'munsi

  • *

    Pafupifupi makilomita 296. Sitadiya imodzi ndi yofanana ndi mamita 185. Onani Zakumapeto B14.

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 212-214

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 14:1Yoh 1:29; Chv 5:6; 22:3
Chiv. 14:1Sl 2:6; Ahe 12:22; 1Pe 2:6
Chiv. 14:1Chv 7:4
Chiv. 14:1Chv 3:12
Chiv. 14:3Sl 33:3; 98:1; 149:1; Chv 5:9
Chiv. 14:3Chv 4:6
Chiv. 14:3Chv 4:4; 19:4
Chiv. 14:3Chv 7:4
Chiv. 14:42Ak 11:2; Yak 1:27; 4:4
Chiv. 14:41Pe 2:21
Chiv. 14:41Ak 6:20; 7:23; Chv 5:9
Chiv. 14:4Yak 1:18
Chiv. 14:5Aef 5:25-27; Yuda 24
Chiv. 14:6Mt 24:14; Mko 13:10; Mac 1:8
Chiv. 14:72Pe 2:9
Chiv. 14:7Eks 20:11; Sl 146:6
Chiv. 14:8Chv 17:18
Chiv. 14:8Yes 21:9; Chv 18:21
Chiv. 14:8Yer 51:7, 8; Chv 17:1, 2; 18:2, 3
Chiv. 14:9Chv 13:1
Chiv. 14:9Chv 13:15, 16
Chiv. 14:10Sl 75:8; Chv 11:18; 16:19
Chiv. 14:10Chv 21:8
Chiv. 14:11Mt 25:46; 2At 1:9; Chv 19:3
Chiv. 14:11Chv 13:16-18; 16:2; 20:4
Chiv. 14:12Ahe 10:38
Chiv. 14:12Chv 13:10
Chiv. 14:131Ak 15:51, 52; 1At 4:16, 17
Chiv. 14:14Da 7:13
Chiv. 14:15Mt 13:30
Chiv. 14:18Yow 3:13
Chiv. 14:19Chv 19:11, 15
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 14:1-20

Chivumbulutso Chimene Yohane Analandira

14 Kenako ndinayangʼana ndipo ndinaona Mwanawankhosa+ ataimirira paphiri la Ziyoni.+ Iye anali limodzi ndi enanso 144,000+ amene analembedwa dzina lake ndi dzina la Atate+ wake pazipumi zawo. 2 Ndiyeno ndinamva phokoso kuchokera kumwamba ngati mkokomo wa madzi ambiri ndiponso ngati phokoso la bingu lamphamvu. Phokoso ndinamvalo linali ngati la oimba amene akuimba pogwiritsa ntchito azeze awo. 3 Iwo ankaimba nyimbo imene inkamveka ngati nyimbo yatsopano+ pamaso pa mpando wachifumu, pamaso pa angelo 4+ ndi pamaso pa akulu.+ Palibe amene anatha kuphunzira nyimboyo kupatulapo 144,000+ amene anagulidwa padziko lapansi. 4 Amenewa ndi amene sanadzidetse ndi akazi ndipo ali ngati anamwali.+ Iwo ndi amene amatsatira Mwanawankhosa kulikonse kumene akupita.+ Iwowa anagulidwa+ pakati pa anthu ngati zipatso zoyambirira+ zoperekedwa kwa Mulungu ndi kwa Mwanawankhosa. 5 Mʼkamwa mwawo simunapezeke chinyengo ndipo alibe chilema.+

6 Ndinaona mngelo wina akuuluka chapafupi mumlengalenga. Iye anali ndi uthenga wabwino wosatha woti aulengeze kwa anthu amene akukhala padziko lapansi, kudziko lililonse, fuko lililonse, chilankhulo chilichonse ndi mtundu uliwonse.+ 7 Iye ankanena mofuula kuti: “Opani Mulungu ndi kumupatsa ulemerero chifukwa ola lakuti apereke chiweruzo lafika.+ Choncho lambirani Iye amene anapanga kumwamba, dziko lapansi, nyanja+ ndi akasupe amadzi.”

8 Kenako mngelo wachiwiri anamutsatira ndipo anati: “Wagwa! Babulo Wamkulu+ wagwa,+ amene anachititsa kuti mitundu yonse ya anthu imwe vinyo wa chilakolako cha* chiwerewere* chake!”+

9 Mngelo wina wachitatu anawatsatira ndipo ankanena mofuula kuti: “Ngati wina walambira chilombo+ ndi chifaniziro chake ndipo walandira chizindikiro pachipumi kapena padzanja lake,+ 10 adzamwanso vinyo wosasungunula wa mkwiyo wa Mulungu amene akuthiridwa mʼkapu ya mkwiyo wake.+ Ndipo adzazunzidwa ndi moto ndi sulufule+ pamaso pa angelo oyera komanso pamaso pa Mwanawankhosa. 11 Ndipo utsi wa kuzunzidwa kwawo udzafuka mpaka kalekale.+ Amene akulambira chilombo ndi chifaniziro chake ndiponso aliyense amene walandira chizindikiro cha dzina lake, adzazunzidwa masana ndi usiku osapuma.+ 12 Apa mʼpamene oyerawo, amene akusunga malamulo a Mulungu ndi kutsatira chikhulupiriro+ cha Yesu, akufunika kupirira.”+

13 Kenako ndinamva mawu kuchokera kumwamba akuti, “Lemba kuti: Osangalala ndi anthu amene akufa ali ogwirizana ndi Ambuye+ kuyambira pa nthawi ino kupita mʼtsogolo. Mzimu ukuti asiyeni apume ku ntchito yawo imene anaigwira mwakhama, chifukwa zimene anachita zikupita nawo limodzi.”

14 Kenako ndinayangʼana ndipo ndinaona mtambo woyera. Pamtambopo panali patakhala winawake wooneka ngati mwana wa munthu,+ atavala chisoti chachifumu chagolide kumutu kwake ndipo mʼdzanja lake munali chikwakwa chakuthwa.

15 Mngelo wina anatuluka mʼnyumba yopatulika yapakachisi akulankhula mofuula kwa amene anakhala pamtambo uja kuti: “Tsitsa chikwakwa chako nʼkuyamba kumweta, chifukwa ola lomweta lafika ndipo zokolola zapadziko lapansi zakhwima.”+ 16 Choncho amene anakhala pamtambo uja anatsitsira chikwakwa chake chija padziko lapansi mwamphamvu ndipo anamweta zokolola zapadziko lapansi.

17 Mngelo winanso anatuluka mʼnyumba yopatulika yapakachisi amene ali kumwamba, nayenso anali ndi chikwakwa chakuthwa.

18 Mngelo winanso anatuluka kuguwa lansembe ndipo anali ndi ulamuliro pa moto. Iye analankhula mofuula ndi mngelo amene anali ndi chikwakwa chakuthwa uja kuti: “Tsitsa chikwakwa chako chakuthwacho nʼkumweta mpesa wapadziko lapansi ndipo usonkhanitse pamodzi maphava ake chifukwa mphesazo zapsa.”+ 19 Mngeloyo anatsitsira chikwakwa chake padziko lapansi mwamphamvu nʼkumweta mpesa wapadziko lapansi. Kenako anauponya mʼchoponderamo mphesa chachikulu cha mkwiyo wa Mulungu.+ 20 Anapondaponda mopondera mphesamo kunja kwa mzinda ndipo magazi anatuluka mʼchoponderamo mphesacho mpaka kufika mʼzibwano za mahatchi, nʼkuyenderera mtunda wa masitadiya 1,600.*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena