Zosonyezera
Zosonyezera zimenezi sizikuphatikiza mbali iriyonse ya ndandanda ya nkhani yaikulu iriyonse. Kuti mupeze mfundo zina, tembenukirani ku mu(mi)tu wo(yo)yenelera m’masamba a mmbuyomu ndi kuŵerenga mitu yankhani yaing’ono.
Abrahamu, akazi ake, 385
Adamu ndi Hava, 25-27
anali anthu enieni, 25, 26, 106
chifukwa chake timavutika ndi zimene Adamu anachita, 223-225
dipo la mbadwa zawo, 123, 124 kodi anapita kumwamba?, 204
tchimo—kodi ndilo “kakonzedwe” ka Mulungu?, 27, 118
tchimo, mmene liliri lothekera, 358
ukwati, 384
Akazi, aminisitala, 29
Baibulo silimaŵasonyeza kukhala anthu apansi, 27-29
chophimba kumutu, 29, 30
mafuta osalalitsa khungu ndi majuwelo, 31
Akristu
mmene mungadziŵire owona, 89, 90, 167, 168, 287
ndiwo mboni za Yehova ndi za Yesu, 280
Akuda, themberero pa Kanani, 236, 237
Akufa, chiukiriro chawo, 80, 109-114, 379, 380
kulankhula nawo, 154, 155, 189, 190-192
kumene iwo ali, 152, 153
maholide owakumbukira, 244, 245
sangathandize kapena kuvulaza amoyo, 188
ubatizo wao, 366, 367
Alefa ndi Omega, 399
“Amayi wa Mulungu,” Mariya, 256, 257
Aminisitala, akazi, 29
Ana, 10
ana a Mulungu, 237
kubadwa opunduka, 226
kupoperedwa mwazi, 317
lingaliro la Mulungu pa osabadwa, 211
pa Armagedo, 40, 41
ubatizo wa makanda, 364, 365
Ana Aamuna a Mulungu, 158, 237
Aneneri, kudziŵikitsa owona ndi onama, 32-35
Aneneri Onyenga, 32-37
kodi ndiwo Mboni za Yehova?, 36, 37
idziŵikitsidwa, 37, 38
kumene imenyedwera, 38, 39
opulumuka, 40
Atumwi, kukhululukira machimo, 219
Petro, “thanthwelo”?, 196-198
Ayuda, 42-47
chiŵerengero cha 144 000, 208, 209
kodi ndiwo anthu osankhidwa?, 42-44
kukanidwa kwa Yesu monga Mesiya, 425
kuwachitira umboni, 22, 23
Babulo, chisonkhezero chachipembedzo lerolino, 49, 50
kuulula, 219, 220
maloto, 247
milungu yautatu, 49
mtanda, 304, 305
Petro m’Babulo, 199
Babulo Wamkulu, akudziŵikitsidwa, 47-51
kuthaŵa kofulumira, 51
kudalirika kwa matembenuzidwe, 57, 58, 328
kuliŵerenga nokha nkosakwanira, 89, 93, 94
maumboni a kuuziridwa, 54, 55
Boma, 62-66
chifukwa chake ulamuliro waumunthu umalephera kukhutiritsa, 62-65
lingaliro la Akristu ku ladziko, 368, 369
Ufumu wa Mulungu, 64-66, 375, 376
Chaka Chatsopano, mapwando ake, 243
Chakudya, chochuluka mu Ufumuwo, 378
mnofu wanyama, 314
Chikhululukiro
atumwi analolezedwa kukhululukira, 219
Chikhulupiriro, 67-70
chifukwa chake siyense amene ali nacho, 67, 68
chikhulupiriro chokha nchosakwanira, 70, 97
mmene chingapezedwere, 68, 69
Chikondi, cha Mulungu, kodi chikaswedwa ndi Armagedo?, 41
cha pa munthu mnzathu, 88
chizindikiro cha chipembedzo chowona, 90
kusoŵeka m’dziko, 11
kuzirala, 264
Chikumbutso, akudya, 72
deti, 73, 74
kuchuluka kwa nthaŵi za kuchitika, 73, 74, 283, 284
tanthauzo, 70, 71
zizindikiro, 71, 72
Chilamulo cha Mose, kuchotsedwa, 348, 349
mbali “zadzoma” ndi “zamakhalidwe,” 347, 348
Chilango, chilango chamuyaya?, 146-149
kodi nsautso ndizo chilango cha Mulungu?, 227, 228
pambuyo pa imfa?, 344
Chilekaniro, chaukwati, 385, 386
Chilengedwe, 74-78
kuchikhulupilira, m’gawo lasayansi, 74-76
kufanana mumpangidwe, 77
magwero a zipangizo, 77, 78
nthaŵi yophatikizidwa, 78
Chilengedwe chonse, magwero ake, 56
Chilimbikitso, 79-82
Chimwemwe, 11, 62, 63, 204, 205
Chinjoka, chinalankhula kwa Hava, 26
Chipanduko, 325
Chipembedzo, 83-94
Babulo Wamkulu, 47-52
chifukwa chake kuli zipembedzo zambiri motero, 83
chimene chimapatula Mboni za Yehova, 270-272
cholinganizidwiratu, 87-88
chipembedzo chimodzi chokha chowona, 93, 275
kodi m’zonse muli abwino? 84, 85, 92, 93
kuchoka m’chipembedzo chamakolo, 85, 86
kuloŵana chikhulupiliro, 86, 87
mmene mungadziŵire chowona, 89, 90
Chipulumutso, 94-99
Ayuda, 44
kodi chiri cha awo amene saali “obadwanso”?, 159
kodi mutapulumitsidwa kamodzi mwapulumutsidwa nthaŵi zonse?, 96
kodi ncha anthu onse?, 94-96
Chisangalalo, kuchilondola, 248, 249, 325, 326
Chisautso chachikulu, opulumuka, 216, 267, 268
Chisinthiko, 99-106
“anthu onga anyani” ojambulidwa, 103
cholembedwa cha zokwiriridwa zakale, 101, 102
dongosolo loŵerengera zaka, 229, 230
kodi chinagwiritsiridwa ntchito ndi Mulungu?, 76, 77, 105, 106
kodi chiri chausayansi?, 99, 100
kusavomerezana pakati pa asayansi, 100
masinthidwe, 102
Chisoni, pa imfa ya wokondedwa, 155
Chisudzulo, 386, 387
Chitaganya
mkhalidwe wa Mboni za Yehova kulinga ku kuwongolera, 278, 279
Chitsenderezo, mpumulo wanthaŵi zonse, 63, 64
Chiukiriro, 107-114
cha kumwamba, 109
cha padziko lapansi, 110-114
kusiyana ndi kudziveka thupi, 177, 178
thupi loukitsidwa la Yesu, 107-109, 431
Chiukiro, 64
Chiwawa, 326
Chiweruzo, chiukiriro cha, 111
Chizunzo, chifukwa chake Mboni zimazunzidwa, 265, 278
chilimbikitso cha kupilira, 80, 81
‘Chizunzo chamuyaya,’ 146-149
kodi chimaikiratu “nthaŵi ya kufa”?, 114
kodi chinthu chirichonse chinadziŵidwiratu ndi kulinganizidwiratu ndi Mulungu?, 116-120
kodi chinthu chiri chonse “ndicho chifuniro cha Mulungu,”? 115, 116
Cholinganizidwiratu, Adamu, 118
Akristu, 119, 120
ndicho “chifuniro cha Mulungu,” 115, 116
Yakobo ndi Esau, 119
Yudase Iskariote, 119
(Wonaninso “Choikidwiratu.”)
Chophimba kumutu, chifukwa chake chiri chofunika, 29, 30
Chowonadi, chowonadi chenicheni, 60, 61, 136, 137
Chuma, kudziwonetsera, 326
moyo wolamuliridwa ndi kuchikhumba, 326
Dipo, 121-127
ana, 226
chifukwa chake liri lofunika, 122-124
kodi liri ndi chiyambukiro chotani panjira imene tikugwiritsira ntchito miyoyo yathu?, 127
mmene imfa ya Yesu inaliri yosiyana, 122
opindulawo, chifukwa chake, 124-126
Dziko, 128-131
kuphatikizidwa kwachipembedzo, 50, 202
kutembenuzidwa, 381, 382
kutetezeredwa ku mzimu wake, 323-327
mkhalidwe wa Akristu kulinga ku, 90, 130, 272, 374
opulumuka mapeto, 267, 268
tanthauzo la mikhalidwe, 53, 261-266
wolamulira, 128, 129, 355, 356
dziko lapansi kukhalabe kosatha, 37, 38, 131-133
kukhalapo ndi moyo wamuyaya, 207, 208
mpangadwe wa planeti, 56
ngati anthu sakafa, kodi munthu aliyense adzakhala kuti?, 113, 114, 135
nzika zake—kodi zidzabwerera kuchokera kumwamba?, 134, 217
opulumukirapo, pambuyo pa chimariziro cha dziko, 215, 216, 267, 268
Paradaiso wamtsogolo, 336-342, 380
umboni wa chilengedwe, 75
Esau, kodi anaikidwiratu?, 119
Filosofi, 136-139
Fodya, 251-254
Gehena, 148, 149
Gulu, 139-143
kodi nlofunika?, 87, 88
mmene mungadziŵire lowoneka la Mulungu, 143
umboni wakuti Mulungu ali nalo, 139-142
Helo, 144-151
amene amapitako, 145
‘chizunzo chamuyaya,’ m’Chivumbulutso, 147, 148
Gehena, 148, 149
munthu wachuma ndi Lazaro, 149, 150
chiyembekezo cha chiukiriro, 80, 109- 114, 379
imfa ya Yesu njosiyana, 122
kodi iri ndi nthaŵi yoikidwiratu?, 114, 156
kodi Mulungu analinganizanji?, 151, 156, 291, 292
kodi pali chilango pambuyo pake?, 146-150, 344
lingaliro la Ababulo, 49
malipoti a “moyo wina,” 153-155
miyambo ya kulira maliro, 155, 156
ya Adamu, kuchotsedwa, 380
yochititsidwa ndi kusuta fodya, 252, 253
Isitala, 242, 243
Israyeli, kukwaniritsidwa kwa ulosi wa Baibulo, 45-47
wauzimu, 46, 47
Kaini, mkazi wake, 235
Kagulu kopanda mwambo, chifukwa chake Mboni siziri, 273
Kalankhula, kochititsidwa ndi kugwidwa ndi mzimu, 285
konyansa, 326
Khamu lalikulu, chiyembekezo cha padziko lapansi, 209
lipulumuka chisautso chachikulu, 216
King James Version, 61, 62
Krisimasi, 239-241
Kubadwanso, 157-161
chifukwa chake kuli kofunikira, 157, 158
ngati simuli wotero, kodi muli ndi mzimu woyera?, 159, 160
ngati simuli wotero, kodi ndinu wopulumutsidwa?, 159
Kubweranso kwa Kristu, 161-165
kosawoneka, 162-164
Kuchiritsa, 166-170
kozizwitsa—kodi kumachitidwa ndi mzimu wa Mulungu lerolino?, 166, 167 170
ngozi m’kukhulupirira mizimu, 169, 192, 193
Kuchitira umboni, 90, 265, 300
kaamba ka Yehova ndi Yesu, 280
kunyumba ndi nyumba, 277
Kudziimira, kodi pali ufulu weniweni popanda miyezo Yabaibulo?, 170-173
mikhalidwe yoti ipeŵedwe, 173, 174
Kudziveka Thupi Lanyama, 174-178
kodi umboni wake, m’Baibulo?, 175-177
malingaliro achilendo a kuzoloŵerana ndi anthu ndi malo, 174, 175
nkosiyana ndi chiyembekezo cha Baibulo, 177, 178
Kudziŵa pasadakhale: wonani
“Choikidwiratu.”
kugonana kwa aziŵalo zofanana, 180-183
kunja kwa ukwati, 180
lingaliro la Baibulo, 179, 180
Kugonana kwa aziŵalo zofanana, 180-183
Kuikidwa mwazi, ana, 317
kugwiritsiridwa ntchito kwa mwazi wa anthu, 315
zoloŵa mmalo, 316
chifukwa chake kwachuluka motere, 183, 184
chifukwa chake Mulungu wakulola, 184-187
chifukwa chake pambuyo pa kukhazikitsidwa kwa Ufumu, 233
kodi ndiwo umboni wakuti kulibe Mulungu?, 307, 308
nsautso, kodi ndicho chilango cha Mulungu?, 227, 228
Kukhalapo, kwa Kristu, 161-165, 261-266
Kukhalapo musanabadwe, 203
“Kukhaliridwa pakati kopanda uchimo,” kwa Mariya, 257, 258
Kukoma mtima, 11
Kukondetsa zinthu zakuthupi, 171, 326
Kulambira, chilengedwe chonse chitagwirizanitsidwa, 377
anthu, 327
kugwiritsiridwa ntchito kwa zifanizo, 49, 259, 333, 434-438
mtanda, 305, 306
sikonse kovomerezedwa ndi Mulungu, 83, 84
Yesu, 429
Kulambira mizimu, 190-195
anamgoneka, 248, 249
kodi muli chivulazo chotani m’kufunsira kwa wolankhula ndi mizimu?, 192, 193
kodi nkotheka kulankhula ndi akufa?, 190-192
kupeza chimasuko ku chisonkhezero chake, 195
Kulinganizidwiratu, onani “Choikidwiratu.”
Kulira maliro, a akufa, 155
Kuloŵa Mmalo Kwautumwi, 196-203
kodi Petro anali ku Roma?, 199
“mfungulo za ufumu,” 198, 199
mzera wa kuloŵa mmalo, 200
Petro, kodi ndiye “thanthwelo”?, 196, 197
Kuloŵana chikhulupiliro, 86, 87
Kumizidwa, 364
Kumwamba, 203-210
amene amapitako, 203-206, 208, 209
chifukwa chake ena amapita kumwamba, 109, 210
chiŵerengero cha opita kumwamba, 208, 209
kodi awo otengeredwa kumwamba adzabwereranso kudziko lapansi?, 134, 217
‘kutsika kwa Ambuye kuchokera kumwamba,’ 214
kutengedwa m’thupi, 212-218
matupi a anthu kumwamba, 107-110, 214, 215, 431
pamene Akristu atengeredwa kumwamba, 212-217
thupi la Mariya, 258
Kunyada, 325
Kupenda nyenyezi, 50, 120, 121, 240
Kupereŵera kwa chakudya, m’masiku otsiriza, 262, 263
Kupezedwa kwa nyumba, 12, 13, 65, 378
Kusakhoza kufa,
magwero a chiphunzitso cha Dziko Lachikristu, 298, 299
miyoyo ya anthu siiri yosakhoza kufa, 153, 188, 297
Kusayeruzika, m’masiku otsiriza, 264
Kusiyana kwa atsogoleri achipembedzo ndi anthu wamba, 50
Kusuta fodya, 251-254
Kutaya mimba, 210-212
Kutaya mtima, 79-82
Kutembenuka, Ayuda, 44, 45
ufumu sukayembekezera kutembenuzidwa kwa dziko, 381, 382
Kutengedwa m’Thupi, 212-218
Kuthiriridwa mwazi, kusala mwazi, 313-315, 317, 318
mankhwala oloŵa mmalo, 316
Kutsenderezeka, mpumulo wosatha, 63-65
Kuulula, 218-222
Kuunika kozungulira mutu, 333, 334
Kuuziridwa, umboni m’Baibulo, 54-57
amene ali ndi thayo lake, 116, 222, 223
ana obadwa opunduka, 226
chifukwa chake Mulungu wakulola, 222-229
kodi ndiko kumene Mulungu analinganiza?, 292
kodi ndiko umboni wakuti kulibe Mulungu?, 307, 308
Kuŵerengera zaka
‘nthaŵi zoikidwiratu za amitundu,’ 231-233
Kuwombeza, maseŵero, 193, 194
Madeti, kuŵerengera 1914, 231-233
njira za asayansi zoŵerengera zaka, 229, 230
nyengo za Chigumula chisanakhale za anthu, 230, 231
Mafuko a anthu, 234-239
magwero a akuda, 236, 237
zifukwa za mikhalidweyo, 235, 236
Mafuta osalalitsa khungu, ogwiritsiridwa ntchito ndi akazi, 31
Maholide, Chaka Chatsopano, 243
Isitala, 242, 243
Krisimasi, 239-241
maholide amtundu, 246
okumbukira “mizimu ya akufa,” 244, 245
Tsiku la Amayi, 245
Tsiku la Valentine, 245
Majini, kodi ndiwo mfungulo ya chisinthiko?, 102
Majuwelo, ogwiritsiridwa ntchito ndi akazi, 31
Makanda, imfa ya, 152
kupunduka kobadwa nako, 226
ubatizo, 364, 365
Makolo akale, akufa, sangathe kuthandiza kapena kuvulaza, 188
kuŵakonda adakali amoyo, 189
mauthenga ochokera kwa akufa?, 153, 155, 189
Malamulo Khumi, anachotsedwa, 348, 349
Malodza abwino, 193, 194
Maloto, 246, 247
Mankhwala (Anamgoneka), chamba, 250, 251, 253
fodya, 251-253
kuwonjoka ku, 253, 254
malamulo amakhalidwe abwino Abaibulo, 248, 249, 251-253
ziyambukiro, 250-253
Mantha, owopa akufa, 188
owopa Yehova, 422, 423
masiku otsiriza, 264, 265
Maplaneti, kodi pali moyo pa enawo?, 294
Mariya (Amayi ŵa Yesu), 254-261
kodi anakhaliridwa pakati popanda uchimo?, 257, 258
kodi ndiye “Amayi ŵa Mulungu,” 256, 257
kodi thupi lake laumunthu liri kumwamba?, 258
kulambiridwa, 259, 260
kupemphera kwa Mariya, 258, 259
Maseŵero, oloŵetsamo kuwombeza, 193, 194
chifukwa chake akhalako kwanthaŵi yaitali motero, 268
chiyambi, mu 1914, 266, 267
tsopano ali mkati, 261-266, 268, 269
Masinthidwe, chisinthiko, 102, 103
Matembenuzidwe, kudalirika kwa Baibulo, 57, 58, 328
pamene mamasuliridwe a Baibulo asiyana, 402, 403
Matenda, kuchiritsa kosatha, 79, 169, 170, 378
kuchiritsa mwachikhulupiliro, 166, 167, 170
Matsenga, 50
Mavesi, a Baibulo—chifukwa chake ena akuwonekera kukhala osoŵeka, 329
Mayanjano, oipa, 172
Mbendera, lingaliro Lachikristu, 372, 373
Mboni za Yehova, 270-280
chifukwa chake zimazunzidwa, 278
kodi ndizo chipembedzo cha ku America?, 272
kodi ndizo chipembedzo chowona chokha?, 275
kulungamitsa malingaliro, 35, 36, 277
mmene ntchito yawo imalipiliridwira, 273
sindizo aneneri onyenga, 36, 37
zikhulupiriro zimene zimazilekanitsa, 270-272
ziyambi, 274
Mbudha, kumchitira umboni, 21, 22
Mdyerekezi, 352-357
Mesiya, chifukwa chake Ayuda anakana Yesu, 425, 426
Mfungulo za Ufumu, 198, 199
Mhindu, kumchitira umboni, 22
Mikayeli, akudziŵikitsidwa, 432, 433
Misa, kodi imapereka mpumulo ku miyoyo m’purigatoriyo?, 284
kuchuluka kwa nthaŵi za kuchitidwa, 283, 284
kusandulizidwa kukhala thupi lenileni ndi mwazi weniweni, 280-282
nsembe, 280-283
Mitala, 384, 385
Mitambo, “kudza m’mitambo” kwa Yesu, 163, 164, 214
‘kukwatulidwa m’mitambo,’ 212, 213
Mkazi, kodi angakhale woposa mmodzi?, 384, 385
mbali yake m’banja Lachikristu, 28, 29
Mliri, masiku otsiriza, 264
M’Malirime kulankhula, 284-289
kodi mphatsoyo idzapitirizabe kwautali wotani? 287, 288
kodi ndiwo umboni wakuti munthuyo ali ndi mzimu woyera?, 285, 286
Mngelo Wamkulu, Yesu Kristu, 432, 433
Moto, kodi dziko lapansi lidzawonongedwa ndi moto?, 132-134
kubatizidwa nawo, 367, 368
Moto wa helo, magwero a chiphunzitsocho, 150, 151
Moyo (Life), 289-294
chiyambukiro chimene dipo liyenera kukhala nacho pa wathu, 127
kusauchitira ulemu, 248, 251-253
kutaya mimba, 210-212
moyo wamuyaya, 11, 12, 72, 73, 122-124, 207, 208, 292, 293
pa maplaneti ena?, 294
Moyo (Soul), chimene uwo uli, 294, 296
chiukiriro, 107
kusakhoza kufa—magwero a chiphunzitsocho, 154, 298, 299
kudziveka thupi, 174-179
ngwosiyana ndi mzimu, 297, 298
Mpatuko, 299-302
mkhalidwe kulinga kwa ampatuko, 301
zizindikiro zoŵadziŵira, 300, 301
Mphatso za mzimu, chifukwa chake zinaperekedwa, 169
Mpulumutsi, Yehova, 400
Yesu Kristu, 390, 391, 400, 433, 434
Msilamu, kumchitira umboni, 23, 24
Mtanda, imfa ya Yesu, 302, 303
kuulambira, 305, 306
magwero a wa Dziko Lachikristu, 304, 305
Mtengo, imfa ya Yesu, 302, 303
Mtsogolo, chifukwa chake simuyenera kutembenukira ku mizimu, 193,
chimene Baibulo limaneneratu za, 12 116, 117, 376-381, 389, 390
dzina lake—kumene limapezeka m’matembenuzidwe Abaibulo, 415-419
“Mulungu wowona yekha,” 311, 397, 398
munthu weniweni, 309
umboni wa kukhalako, 307, 308, 312, 313
wopanda chiyambi, 309, 310
Yesu monga mulungu, 311, 397, 398, 400, 403, 404, 426-428
(Wonaninso “Yehova.”)
Mwazi, 313-319
Mzimu, kudziŵa awo amene ali ndi mzimu woyera, 159, 160, 285-287, 320, 321, 323
mphamvu yogwira ntchito ya moyo
—chimene chimaichitikira pa imfa, 297, 298, 321-323
mphamvu yogwira ntchito ya Mulungu, 319, 320, 393, 394, 398
ubatizo, 366-368
Mzimu wadziko, mikhalidwe, 323-327
Mzimu woyera: wonani “Mzimu.”
Namwali, Mariya, 255, 256
Ndale zadziko, kuloŵetsedwamo kwachipembedzo, 50
mkhalidwe wa Akristu, 371, 372
New World Translation, 327-331
dzina la Yehova m’Malemba Achikristu Achigiriki, 329
mavesi owonekera kukhala osoŵeka, 329
mtundu wa matembenuzidwe, 327, 328
otembenuza, 328
1914, kukhazikitsidwa kwa Ufumu, 231-233
lingaliro la olemba mbiri yadziko, 266, 267
Njala, m’masiku otsiriza, 262, 268
Nkhondo, ya Armagedo, 37-42
lingaliro Lachikristu, 369-371
m’masiku otsiriza, 261, 262
mu Israyeli wakale, 370
Tchalitchi cha Katolika, 202, 203
Nsautso, kodi ndizo chilango chochokera kwa Mulungu?, 227, 228
Ntchito, zogwirizana ndi chikhulupiliro, 70, 97
Ntchito yolembedwa, Ufumu udzagaŵira, 12, 13, 65, 378
“Nthaŵi zoikidwiratu za amitundu” mmene zimaŵerengedwera, 231-233
Nyenyezi, kupenda nyenyezi, 50, 120, 121
nyenyezi inatsogolera openda nyenyezi kwa Herode, 240, 241
Nyimbo zautundu, lingaliro Lachikristu, 372, 373
Nzeru, yaumunthu, 137-139
yowona, 136
Obwebweta, mauthenga ochokera kwa akufa, 189, 191, 192
Ogwidwa ndi mzimu, 166, 167, 285, 286
Oyera mtima, 331-335
kodi ali opanda uchimo uliwonse?, 334
kupemphera kwa, 332, 333
kuunika kokweteza mutu, 333, 334
zifanizo ndi zinthu zakale zopatulika, 333, 435, 436
Paradaiso, 335-339
wa padziko lapansi, 336, 380, 381
wochita zoipa m’Paradaiso, 337-339
Pemphero, 339-342
kwa Mariya, 258, 259
kwa “oyera mtima,” 332, 333
mapemphero a amene Mulungu amamva, 339, 340
mapemphero a amene Mulungu samavomereza, 340, 341
nkhani zoyenelera, 341, 342
Petro, Apapa sindiwo oloŵa mmalo ake, 200
kodi anali ku Roma kapena ku Babulo?, 199
‘mfungulo za ufumu,’ 198, 199
“thanthwelo”?, 196, 197
Phompho, Satana kubindikiritsidwamo, 356, 357
Purigatoriyo, 343-345
magwero a chiphunzitsocho, 343
Misa ya okhalamo, 284
Sabata, 345-351
lamlungu ndi mlungu, kodi nla Akristu?, 345, 346
tanthauzo kwa Akristu, 349-351
Satana Mdyerekezi, akugubitsa anthu kumka ku Armagedo, 41, 42
ali ndi thayo la kuipa, 183, 184
anaponyedwa kuchokera kumwamba, 233, 356, 357
chifukwa chake waloledwa kukhalako, 354, 355
chiyambi, 354
kuponyedwa kuphompho, 356, 357
mulungu wa dongosolo lino, 355, 356
ndiye wolamulira wadziko, 355, 356
Sauli, analankhula ndi “Samueli” kudzera mwa mkazi wobwebweta, 191
Sayansi, Baibulo liri patsogolo pa zotulukiridwa ndi asayansi, 56, 57
imakhulupilira chilengedwe, 74-76
imakhulupilira Mulungu, 307
malingaliro otsutsana onena za chisinthiko, 99, 100
Solomo, akazi, 384, 385
Tchimo, chikhululukiro, 219, 365, 366
chiyambukiro pa unansi ndi Mulungu, 361
kodi lerolino kuli tchimo?, 359, 360
kodi oyera mtima alibe?, 334
kuulula, 198, 199
kuyeretsedwa ku, 344, 345, 365, 366
la Adamu, kodi ndilo ‘kulinganiza’ kwa Mulungu? 27, 118
Mariya, kodi analibe tchimo?, 257, 258
mmene lirili lotheka kwa cholengedwa changwiro, 358, 359
ladala, 218, 219, 221, 222, 358
Thanthwe, Kristu, osati Petro, 196, 197
Themberero, fuko la akuda?, 236, 237
Thupi la munthu, linalinganizidwira kukhalako kosatha, 293
umboni wa chilengedwe, 75, 76
Tsiku, utali wa la kulenga, 78, 103, 104
Tsiku la Amayi, 245
Tsiku la kubadwa, 361-363
Tsiku la Valentine, 245
Ubatizo, kumizidwa m’madzi, 364-366
ndi moto, 367, 368
ndi mzimu woyera, 366-368
“wa akufa,” 366, 367
Uchete, 368-374
kuphatikizidwa m’ndale zadziko, 371, 372
mbendera ndi nyimbo zautundu, 372-374
nkhondo yazida, 369-371
boma, 375, 376
chimene udzakwaniritsa, 376-381
“mfungulo za ufumu,” 198, 199
nthaŵi ya kukhazikitsidwa, 231-233, 381, 382
olamulira limodzi ndi Kristu, 157, 158, 208-210
Ukwati, chilekaniro, 385, 386
chisudzulo, 386, 387
kugonana usanachitike, 180
kulembetsedwa mwalamulo, 383, 384
mbale ndi mlongo, 387
mitala, 384, 385
mmene mungawongolere, 388
Ulamuliro, nkhaniyo, 184-186, 354, 355
ufumuwo umachirikiza wa Yehova, 376
chifukwa chake muyenera kukhala wokondwerera kwambiri, 390, 391
kukwaniritsidwa, 54-56, 65, 66, 231-233 261-266
umene sunakwaniritsidwebe, 389, 390
Umbeta, 201, 202
Umodzi, wa chilengedwe chonse m’kulambira, 377
wa mafuko onse, 238, 239
Umutu, 28, 29
Upandu, 14
kuwonjezerekako kuli kwenikweni, 264
Utatu, 391-413
kodi malemba ogwiritsiridwa ntchito ndi okhulupilira utatu amapereka maziko olimba? 398-411
kodi malingaliro aakulu ophatikizidwa m’chiphunzitsochi ngogwirizana ndi Baibulo?, 393-398
magwero a chiphunzitsocho, 49, 200, 201, 392, 393
mkhalidwe wa owumamatira, 411, 412
Wachuma ndi Lazaro, fanizo, 149, 150
144 000, chiŵerengero chenicheni, 209
kodi ncha Ayuda akuthupi okha?, 208, 209
kodi ndiwo amene adzapulumuka okha?, 98, 99
Wochita zoipa, lonjezo la Paradaiso, 337, 339
Wokana Kristu, 414, 415
Yahweh, kodi ndiye Yehova kapena Yahweh?, 419, 420
Yakobo, akazi, 384, 385
kodi analinganizidwiratu?, 119
Yehova, 415-423
alibe chiyambi, 309, 310
dzinalo—kumene limapezeka m’Mabaibulo osiyanasiyana, 415-417
dzinalo m’Malemba Achikristu Achigiriki, 329, 418, 419
kodi ndilo dzina la Yesu mu “Chipangano Chakale”?, 421, 422
kodi ndiye Yahweh kapena Yehova?, 419, 420
kufunika kwa dzinalo, 420, 421
kuyeretsedwa kwa dzina lake, 376
Mulungu wowona yekha, 311, 397, 398, 400, 403, 404
(Wonaninso “Mulungu.”)
Yesu Kristu, 423-434
“Adamu wotsirizira,” 26, 123, 124
“akudza m’mitambo,” 163, 164, 214
anabadwa mwa namwali, 255
chifukwa chake Ayuda ambiri sanamlandire, 425, 426
chikumbutso cha imfa yake, 70-74, 282, 283
chiukiriro chathupi, 108, 109, 431, 432
imfa, 122
kodi imfa yake inali pamtengo kapena pamtanda?, 302, 303
kodi iye anali kokha munthu wabwino? 424
maina aulemu a Yehova anagwira ntchito kwa iye, 399, 400
Malemba Achihebri amene amalankhula za Yehova ndi amene anagwira ntchito kwa Yesu, 401
Mpulumutsi, 390, 391, 400, 430, 433, 434
waumulungu osati Mulungu, 403, 404, 426, 427
munthu weniweni, 423, 424
“thanthwe,” 196
umulungu, 413
‘woyamba wa chilengedwe,’ 394, 395
Yehova sindilo dzina lake, 421, 422
ziphunzitso zapamwamba, 138
zochitika zogwirizanitsidwa ndi kukhala pafupi kwake, 162, 165, 261-266
Yudase Iskariote, kodi analinganizidwiratu?, 119
Zakumwa zoledzeretsa
kusiyana kwake ndi chamba, 251
ziyambukiro pa omwererekera nazo, 171, 172
Zifanizo, 434-438
chifanizo kapena fano?, 434-436
kodi zimathandiza m’kulambira?, 435
Mariya, 259
Zachibabulo, 49
za “oyera mtima,” 333, 435, 436
Zigumukire, chifukwa chake Mulungu amalola “zachilengedwe,” 227
Zigumukire zachilengedwe (zotchedwa motero),
chifukwa chake zikuloledwa, 227
Zinyama, kukhetsa mwazi kaamba ka chakudya, 314
miyoyo, 295, 296
paubwenzi ndi anthu, 380
Zivomezi, chifukwa chake Mulungu akuzilola, 227
masiku otsiriza, 263, 268, 269
Ziŵanda, chisonkhezero pa mitundu, 41, 42, 63, 356
kodi zimatenga mpangidwe waumunthu?, 194
kulambira mizimu, 190-195, 352, 353
ziri ndi thayo la kuipa, 183, 184
Zizunzo, wachuma ndi Lazaro, 149, 150
zamuyaya m’Chivumbulutso, 147, 148
Zochiritsa, wonani “Kuchiritsa.”
Zokwiriridwa zakale, chisinthiko, 101, 102
Zosankha, kudalira pa kuŵerenga nyenyezi, 120, 121
kunyalanyaza chifuniro cha Mulungu, 172, 173, 324-327
Zozizwitsa, zamakono, 33, 166, 167