Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 10
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

1 Akorinto 10:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 13:21
  • +Eks 14:22

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2001, tsa. 14

1 Akorinto 10:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ahe 3:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2001, tsa. 14

1 Akorinto 10:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 16:15

1 Akorinto 10:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 17:6; Sl 78:15
  • +Nu 20:11
  • +Mt 16:18; 1Pe 2:4
  • +Yoh 4:10, 25

1 Akorinto 10:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nu 14:16; Eze 20:15; Yuda 5
  • +Nu 14:29; Ahe 3:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2001, tsa. 14

1 Akorinto 10:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nu 11:34; Sl 106:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2010, tsa. 27

    6/15/2001, tsa. 14

    5/15/1999, ptsa. 16-17

    3/1/1995, tsa. 16

1 Akorinto 10:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 32:4
  • +Eks 32:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2010, tsa. 27

    6/15/2001, ptsa. 15-16

    5/15/1999, ptsa. 16-17

    3/1/1995, tsa. 16

1 Akorinto 10:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nu 25:1; 2Pe 2:2
  • +Nu 25:9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’, ptsa. 97-98

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2010, tsa. 27

    4/1/2004, tsa. 29

    6/15/2001, ptsa. 16-17

    5/15/1999, ptsa. 16-17

    3/1/1995, ptsa. 16-17

    7/15/1992, ptsa. 4-5

1 Akorinto 10:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +De 6:16
  • +Nu 21:5
  • +Nu 21:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2010, tsa. 27

    6/15/2001, tsa. 17

    3/1/1995, tsa. 17

1 Akorinto 10:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nu 14:2
  • +Eks 23:21; Nu 14:37

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2010, tsa. 27

    6/15/2001, tsa. 17

    3/1/1995, ptsa. 17-18

1 Akorinto 10:11

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Matanthauzo a Mawu Ena.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 15:4
  • +Ahe 9:26; 1Pe 4:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/1996, ptsa. 17-22

1 Akorinto 10:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Miy 28:14; Lu 22:34; Aro 11:20; Aga 6:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2001, tsa. 11

    7/15/1989, tsa. 11

1 Akorinto 10:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Pe 5:9
  • +1At 5:24; 2At 3:3
  • +Lu 22:32; 2Pe 2:9
  • +1Sa 30:6; Yes 40:29; Mac 27:44; Afi 4:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,

    3/2024, tsa. 4

    4/2019, tsa. 3

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    1/2023, ptsa. 12-13

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    2/2017, ptsa. 29-30

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    4/2016, tsa. 14

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/2015, tsa. 26

    4/15/2014, tsa. 21

    4/15/2012, tsa. 27

    11/15/2010, ptsa. 27-28

    5/15/2009, tsa. 22

    3/15/2008, tsa. 13

    3/15/2001, ptsa. 11-12, 13-14

    6/15/1996, tsa. 11

    10/1/1991, ptsa. 10-11

    3/15/1987, tsa. 29

    Dikirani!, tsa. 26

1 Akorinto 10:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 6:17
  • +De 4:25; Akl 3:5; 1Yo 5:21

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kukambitsirana, tsa. 305

1 Akorinto 10:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 14:20

1 Akorinto 10:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 26:27; Lu 22:17
  • +Mt 26:26; Lu 22:19
  • +1Ak 12:18

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2006, ptsa. 23-24

1 Akorinto 10:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 12:5; 1Ak 12:25
  • +Aef 4:4
  • +Yoh 6:33, 35

1 Akorinto 10:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 9:8
  • +Le 7:15

1 Akorinto 10:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 8:4

1 Akorinto 10:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +De 32:17; Sl 106:37
  • +Yuda 6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2004, tsa. 5

    1/15/1993, ptsa. 22-24

    12/1/1990, tsa. 5

1 Akorinto 10:21

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto 2.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 116:13
  • +Eze 41:22; Mki 1:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 24

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    10/2019, tsa. 30

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1994, ptsa. 8-13

    Kukambitsirana, tsa. 195

1 Akorinto 10:22

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 34:14; De 32:21
  • +Yob 9:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/1987, ptsa. 6-7

1 Akorinto 10:23

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 6:12
  • +Aro 6:14
  • +Aro 14:19; 15:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 35

    Mulungu Azikukondani, ptsa. 84-85

    ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’, ptsa. 72-73

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/1998, tsa. 20

1 Akorinto 10:24

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 10:33; 13:5; Afi 2:21
  • +Afi 2:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 35

    Mulungu Azikukondani, ptsa. 84-85

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    10/2017, tsa. 11

    ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’, ptsa. 72-73

    Lambirani Mulungu, ptsa. 140-141

1 Akorinto 10:25

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ti 4:4
  • +Aro 14:22

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/2010, tsa. 12

    10/15/1992, tsa. 30

1 Akorinto 10:26

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 24:1
  • +Eks 19:5; De 10:14

1 Akorinto 10:27

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 10:8
  • +1Ak 8:7

1 Akorinto 10:28

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 8:10

1 Akorinto 10:29

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 14:16; 1Ak 8:12

1 Akorinto 10:30

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 14:6; 1Ti 4:3

1 Akorinto 10:31

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 5:16; Akl 3:17; 1Pe 4:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 43

1 Akorinto 10:32

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 14:13; 1Ak 8:13; 2Ak 6:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 43

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/2007, tsa. 22

    9/1/1992, ptsa. 21-22

    Lambirani Mulungu, ptsa. 140-141

1 Akorinto 10:33

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 9:22
  • +Aro 15:2; Afi 2:4
  • +1At 2:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 52

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

1 Akor. 10:1Eks 13:21
1 Akor. 10:1Eks 14:22
1 Akor. 10:2Ahe 3:5
1 Akor. 10:3Eks 16:15
1 Akor. 10:4Eks 17:6; Sl 78:15
1 Akor. 10:4Nu 20:11
1 Akor. 10:4Mt 16:18; 1Pe 2:4
1 Akor. 10:4Yoh 4:10, 25
1 Akor. 10:5Nu 14:16; Eze 20:15; Yuda 5
1 Akor. 10:5Nu 14:29; Ahe 3:17
1 Akor. 10:6Nu 11:34; Sl 106:14
1 Akor. 10:7Eks 32:4
1 Akor. 10:7Eks 32:6
1 Akor. 10:8Nu 25:1; 2Pe 2:2
1 Akor. 10:8Nu 25:9
1 Akor. 10:9De 6:16
1 Akor. 10:9Nu 21:5
1 Akor. 10:9Nu 21:6
1 Akor. 10:10Nu 14:2
1 Akor. 10:10Eks 23:21; Nu 14:37
1 Akor. 10:11Aro 15:4
1 Akor. 10:11Ahe 9:26; 1Pe 4:7
1 Akor. 10:12Miy 28:14; Lu 22:34; Aro 11:20; Aga 6:1
1 Akor. 10:131Pe 5:9
1 Akor. 10:131At 5:24; 2At 3:3
1 Akor. 10:13Lu 22:32; 2Pe 2:9
1 Akor. 10:131Sa 30:6; Yes 40:29; Mac 27:44; Afi 4:13
1 Akor. 10:142Ak 6:17
1 Akor. 10:14De 4:25; Akl 3:5; 1Yo 5:21
1 Akor. 10:151Ak 14:20
1 Akor. 10:16Mt 26:27; Lu 22:17
1 Akor. 10:16Mt 26:26; Lu 22:19
1 Akor. 10:161Ak 12:18
1 Akor. 10:17Aro 12:5; 1Ak 12:25
1 Akor. 10:17Aef 4:4
1 Akor. 10:17Yoh 6:33, 35
1 Akor. 10:18Aro 9:8
1 Akor. 10:18Le 7:15
1 Akor. 10:191Ak 8:4
1 Akor. 10:20De 32:17; Sl 106:37
1 Akor. 10:20Yuda 6
1 Akor. 10:21Sl 116:13
1 Akor. 10:21Eze 41:22; Mki 1:12
1 Akor. 10:22Eks 34:14; De 32:21
1 Akor. 10:22Yob 9:4
1 Akor. 10:231Ak 6:12
1 Akor. 10:23Aro 6:14
1 Akor. 10:23Aro 14:19; 15:2
1 Akor. 10:241Ak 10:33; 13:5; Afi 2:21
1 Akor. 10:24Afi 2:4
1 Akor. 10:251Ti 4:4
1 Akor. 10:25Aro 14:22
1 Akor. 10:26Sl 24:1
1 Akor. 10:26Eks 19:5; De 10:14
1 Akor. 10:27Lu 10:8
1 Akor. 10:271Ak 8:7
1 Akor. 10:281Ak 8:10
1 Akor. 10:29Aro 14:16; 1Ak 8:12
1 Akor. 10:30Aro 14:6; 1Ti 4:3
1 Akor. 10:31Mt 5:16; Akl 3:17; 1Pe 4:11
1 Akor. 10:32Aro 14:13; 1Ak 8:13; 2Ak 6:3
1 Akor. 10:331Ak 9:22
1 Akor. 10:33Aro 15:2; Afi 2:4
1 Akor. 10:331At 2:16
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
  • 23
  • 24
  • 25
  • 26
  • 27
  • 28
  • 29
  • 30
  • 31
  • 32
  • 33
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
1 Akorinto 10:1-33

1 Akorinto

10 Tsopano sindikufuna kuti mukhale osadziwa abale, kuti makolo athu akale, onse anali pansi pa mtambo+ ndipo onse anawoloka nyanja.+ 2 Onse anabatizidwa mwa Mose,+ kudzera mwa mtambo ndi mwa nyanja. 3 Ndiponso, onse anadya chakudya chimodzimodzi chauzimu,+ 4 ndipo onse anamwa chakumwa chimodzimodzi chauzimu.+ Pakuti anali kumwa pathanthwe lauzimu+ limene linali kuwatsatira, ndipo thanthwelo+ linatanthauza Khristu.+ 5 Ngakhale zinali choncho, ambiri a iwo Mulungu sanakondwere+ nawo, ndipo anathana+ nawo m’chipululu.

6 Tsopano zinthu zimenezi zinakhala zitsanzo kwa ife, kuti ifenso tisakhale anthu olakalaka zinthu zoipa+ ngati mmene iwo anachitira. 7 Ndipo tisapembedze mafano, mmene ena mwa iwo anachitira,+ monga mmene Malemba amanenera kuti: “Anthu anakhala pansi ndi kudya ndiponso kumwa. Kenako anaimirira n’kuyamba kusangalala.”+ 8 Tisamachite dama,+ mmene ena mwa iwo anachitira dama, n’kufa 23,000 tsiku limodzi.+ 9 Kapena tisamuyese Yehova,+ mmene ena mwa iwo anamuyesera,+ n’kuwonongeka polumidwa ndi njoka.+ 10 Tisakhalenso ong’ung’udza, mmene ena mwa iwo anang’ung’udzira,+ wowonongayo+ n’kuwawononga onsewo. 11 Tsopano zinthu zimenezi zinali kuwagwera monga zitsanzo, ndipo zinalembedwa kuti zitichenjeze+ ifeyo amene mapeto a nthawi* zino atifikira.+

12 N’chifukwa chake amene akuyesa kuti ali chilili asamale kuti asagwe.+ 13 Palibe mayesero amene mwakumana nawo osiyana ndi amene amagwera anthu ena.+ Koma Mulungu ndi wokhulupirika+ ndipo sadzalola kuti muyesedwe kufika pamene simungapirire,+ koma pamene mukukumana ndi mayeserowo iye adzapereka njira yopulumukira+ kuti muthe kuwapirira.

14 Ndiye chifukwa chake, okondedwa anga, thawani+ kupembedza mafano.+ 15 Ndikulankhula nanu ngati anthu ozindikira.+ Dziwani nokha zimene ndikunena. 16 Kodi kapu+ ya dalitso imene timadalitsa, sitanthauza kugawana magazi a Khristu?+ Kodi mkate umene timanyema,+ sutanthauza kugawana thupi la Khristu? 17 Popeza pali mkate umodzi, ifeyo, ngakhale kuti tilipo ambiri,+ ndife thupi limodzi,+ pakuti tonse tikudya nawo mkate umodziwo.+

18 Taganizirani zochitika za Isiraeli wakuthupi:+ Kodi amene amadyako zoperekedwa nsembe sindiye kuti akugawana ndi guwa lansembe?+ 19 Ndiye ndinene chiyani? Kuti choperekedwa nsembe kwa fano chili kanthu, kapena kuti fanolo ndi kanthu?+ 20 Ayi, koma ndikunena kuti zinthu zimene mitundu ina imapereka nsembe imazipereka kwa ziwanda,+ osati kwa Mulungu, ndipo sindikufuna kuti mukhale ogawana ndi ziwanda.+ 21 Sizingatheke kuti muzimwa za m’kapu ya Yehova*+ komanso za m’kapu ya ziwanda. Sizingatheke kuti muzidya “patebulo la Yehova”+ komanso patebulo la ziwanda. 22 Kapena “kodi tikufuna kuputa nsanje+ ya Yehova”? Kodi mphamvu zathu zingafanane ndi zake?+

23 Zinthu zonse ndi zololeka, koma si zonse zimene zili zaphindu.+ Zinthu zonse ndi zololeka,+ koma si zonse zimene zili zolimbikitsa.+ 24 Aliyense asamangodzifunira zopindulitsa iye yekha basi,+ koma zopindulitsanso wina.+

25 Chilichonse chogulitsidwa pamsika wa nyama muzidya+ popanda kufunsa mafunso, poopera chikumbumtima+ chanu, 26 chifukwa “dziko lapansi ndi zonse za mmenemo+ ndi za Yehova.”+ 27 Ngati wina mwa osakhulupirira wakuitanani ndipo mwapita, kadyeni zonse zimene wakupatsani,+ popanda kufunsa mafunso poopera chikumbumtima chanu.+ 28 Koma wina akakuuzani kuti: “Izi zaperekedwa nsembe,” musadye zimenezo poopera amene wakuuzaniyo ndiponso poopera chikumbumtima.+ 29 Sindikunena “chikumbumtima” chako koma cha munthu winayo. N’chifukwa chiyani ufulu wanga ukulamulidwa ndi chikumbumtima cha munthu wina?+ 30 Ngati ndikudya chakudyacho nditayamika Mulungu, kodi ndinyozedwe pa chinthu chimene ndayamikira?+

31 Ndiye chifukwa chake, kaya mukudya kapena kumwa kapena mukuchita china chilichonse, chitani zonse kuti zibweretse ulemerero kwa Mulungu.+ 32 Pewani kukhala okhumudwitsa+ kwa Ayuda, ngakhalenso kwa Agiriki, ndi kwa mpingo wa Mulungu, 33 monga mmene ineyo ndikukondweretsera anthu onse m’zinthu zonse.+ Sikuti ndikungofuna zopindulitsa ine ndekha ayi,+ koma zopindulitsa anthu ambiri, kuti apulumutsidwe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena