Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 16
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la Chivumbulutso

      • Mbale 7 za mkwiyo wa Mulungu (1-21)

        • Anathira padziko lapansi (2), mʼnyanja (3), pamitsinje ndi pa akasupe (4-7), padzuwa (8, 9), pampando wachifumu wa chilombo (10, 11), pa Firate (12-16) ndi pampweya (17-21)

        • Nkhondo ya Mulungu pa Aramagedo (14, 16)

Chivumbulutso 16:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 16:17
  • +Sl 69:24; Zef 3:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 220

Chivumbulutso 16:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 8:7
  • +Chv 13:16, 18
  • +Chv 13:15; 19:20
  • +Eks 9:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 221-223

Chivumbulutso 16:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 8:8
  • +Eks 7:20
  • +Yes 57:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 223-224

Chivumbulutso 16:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 8:10
  • +Eks 7:20; Sl 78:44

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 224-225

Chivumbulutso 16:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 1:4
  • +Sl 145:17; Chv 15:4
  • +De 32:4; Sl 119:137

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Yandikirani, ptsa. 286-288

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 224-225

Chivumbulutso 16:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 79:3
  • +Yes 49:26
  • +Chv 18:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 30-31, 224-225

Chivumbulutso 16:7

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

  • *

    Kapena kuti, “zigamulo.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 6:3
  • +Sl 19:9; 119:137; Chv 19:1, 2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 224-225

Chivumbulutso 16:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 8:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 225-227

Chivumbulutso 16:9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 225, 226-227

Chivumbulutso 16:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 10:21; Yes 8:22

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 227-228

Chivumbulutso 16:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 228-229

Chivumbulutso 16:12

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “kumʼmawa.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 9:13, 14
  • +Yer 50:38
  • +Yes 44:27, 28

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    7/2022, tsa. 6

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2012, ptsa. 17-18

    9/15/1990, tsa. 29

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 229-230, 260-261

    Ulosi wa Danieli, tsa. 281

    Galamukani!,

    12/8/1989, ptsa. 23-26

Chivumbulutso 16:13

Mawu a M'munsi

  • *

    Mʼchilankhulo choyambirira, “mizimu yonyansa.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 12:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 10

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 4

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 230-231

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 18-19

Chivumbulutso 16:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 13:11, 13
  • +Chv 19:19
  • +Yes 13:6; Yer 25:33; Eze 30:3; Yow 1:15; 2:1, 11; Zef 1:15; 2Pe 3:11, 12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 10

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2019, ptsa. 8-9

    Nsanja ya Olonda,

    11/1/2015, tsa. 2

    9/1/2011, tsa. 10

    2/15/2009, tsa. 4

    4/1/2008, tsa. 31

    2/1/2007, tsa. 31

    12/1/2005, tsa. 4

    2/15/1986, tsa. 24

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 230-231, 285-286

    Kukambitsirana, ptsa. 37-42

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 18-20

Chivumbulutso 16:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1At 5:2; 2Pe 3:10
  • +Lu 21:36
  • +Chv 3:18

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 231-232

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2005, tsa. 18

    12/15/2003, tsa. 21

    12/1/1999, ptsa. 18-19

    3/1/1997, ptsa. 14-19

    5/1/1991, tsa. 21

Chivumbulutso 16:16

Mawu a M'munsi

  • *

    MʼChigiriki Haramagedo, kuchokera ku mawu a Chiheberi amene amatanthauza, “Phiri la Megido.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Mb 35:22; Zek 12:11; Chv 19:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2019, ptsa. 8-9

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2137

    Nsanja ya Olonda,

    2/1/2012, ptsa. 5-6

    9/1/2011, tsa. 10

    4/1/2008, tsa. 31

    2/1/2007, tsa. 31

    12/1/2005, tsa. 4

    4/15/1997, tsa. 17

    5/15/1990, tsa. 6

    1/1/1989, ptsa. 16-17

    2/15/1986, tsa. 24

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 232-233, 285-286

    Galamukani!,

    7/8/2005, ptsa. 12-13

    Kukambitsirana, ptsa. 37-42

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 16-20

Chivumbulutso 16:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 16:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 4

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 233-234

Chivumbulutso 16:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 38:19; Da 12:1; Ahe 12:26

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 234

Chivumbulutso 16:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 17:18
  • +Chv 18:2
  • +Yer 25:15; Chv 15:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 234

Chivumbulutso 16:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 6:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 234

Chivumbulutso 16:21

Mawu a M'munsi

  • *

    Mʼchilankhulo choyambirira, “matalente 8.” Onani Zakumapeto B14.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yob 38:22, 23
  • +Eks 9:24

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2020, tsa. 15

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    10/2019, tsa. 16

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2015, tsa. 16

    2/15/2009, tsa. 4

    7/15/2008, ptsa. 6-7

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2242

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 234

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 16:1Chv 16:17
Chiv. 16:1Sl 69:24; Zef 3:8
Chiv. 16:2Chv 8:7
Chiv. 16:2Chv 13:16, 18
Chiv. 16:2Chv 13:15; 19:20
Chiv. 16:2Eks 9:10
Chiv. 16:3Chv 8:8
Chiv. 16:3Eks 7:20
Chiv. 16:3Yes 57:20
Chiv. 16:4Chv 8:10
Chiv. 16:4Eks 7:20; Sl 78:44
Chiv. 16:5Chv 1:4
Chiv. 16:5Sl 145:17; Chv 15:4
Chiv. 16:5De 32:4; Sl 119:137
Chiv. 16:6Sl 79:3
Chiv. 16:6Yes 49:26
Chiv. 16:6Chv 18:20
Chiv. 16:7Eks 6:3
Chiv. 16:7Sl 19:9; 119:137; Chv 19:1, 2
Chiv. 16:8Chv 8:12
Chiv. 16:10Eks 10:21; Yes 8:22
Chiv. 16:12Chv 9:13, 14
Chiv. 16:12Yer 50:38
Chiv. 16:12Yes 44:27, 28
Chiv. 16:13Chv 12:3
Chiv. 16:14Chv 13:11, 13
Chiv. 16:14Chv 19:19
Chiv. 16:14Yes 13:6; Yer 25:33; Eze 30:3; Yow 1:15; 2:1, 11; Zef 1:15; 2Pe 3:11, 12
Chiv. 16:151At 5:2; 2Pe 3:10
Chiv. 16:15Lu 21:36
Chiv. 16:15Chv 3:18
Chiv. 16:162Mb 35:22; Zek 12:11; Chv 19:19
Chiv. 16:17Chv 16:1
Chiv. 16:18Eze 38:19; Da 12:1; Ahe 12:26
Chiv. 16:19Chv 17:18
Chiv. 16:19Chv 18:2
Chiv. 16:19Yer 25:15; Chv 15:7
Chiv. 16:20Chv 6:14
Chiv. 16:21Yob 38:22, 23
Chiv. 16:21Eks 9:24
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 16:1-21

Chivumbulutso Chimene Yohane Analandira

16 Kenako ndinamva mawu ofuula kuchokera mʼmalo opatulika+ akuuza angelo 7 aja kuti: “Pitani, kathireni mbale 7 za mkwiyo wa Mulunguzo padziko lapansi.”+

2 Mngelo woyamba anapita nʼkukathira mbale yake padziko lapansi.+ Atatero, anthu amene anali ndi chizindikiro cha chilombo+ komanso amene ankalambira chifaniziro chake,+ anagwidwa ndi mliri wa zilonda zopweteka+ komanso zoopsa.

3 Mngelo wachiwiri anathira mbale yake mʼnyanja.+ Nyanjayo inasanduka magazi+ ngati a munthu wakufa, moti chamoyo chilichonse mʼnyanjamo chinafa.+

4 Mngelo wachitatu anathira mbale yake pamitsinje ndi pa akasupe amadzi+ ndipo zonse zinasanduka magazi.+ 5 Ndiye ndinamva mngelo amene ali ndi ulamuliro pa madzi akunena kuti: “Inu Mulungu amene mulipo ndi amene munalipo,+ inu Wokhulupirika,+ ndinu wolungama chifukwa mwapereka ziweruzo zimenezi,+ 6 chifukwa iwo anakhetsa magazi a oyera ndi a aneneri+ ndipo inu mwawapatsa magazi kuti amwe.+ Iwo akuyeneradi kulandira chiweruzo chimenechi.”+ 7 Kenako ndinamva guwa lansembe likunena kuti: “Inde, Yehova* Mulungu, inu Wamphamvuyonse,+ ziweruzo* zanu ndi zoona komanso zolungama.”+

8 Mngelo wa 4 anathira mbale yake padzuwa+ ndipo dzuwalo linaloledwa kuwotcha anthu ndi moto. 9 Anthu anapsa ndi kutentha kwakukulu. Koma iwo ananyoza dzina la Mulungu, amene ali ndi ulamuliro pa miliri imeneyi ndipo sanalape nʼkumupatsa ulemerero.

10 Mngelo wa 5 anathira mbale yake pampando wachifumu wa chilombo. Ufumu wa chilombocho unachita mdima+ ndipo anthu anayamba kudziluma malilime chifukwa cha ululu. 11 Koma iwo ananyoza Mulungu wakumwamba chifukwa cha ululu umene ankamva komanso chifukwa cha zilonda zawo ndipo sanalape ntchito zawo.

12 Mngelo wa 6 anathira mbale yake pamtsinje waukulu wa Firate+ ndipo madzi ake anauma,+ kuti njira ya mafumu+ ochokera kotulukira dzuwa* ikonzedwe.

13 Kenako ndinaona mauthenga atatu onyansa ouziridwa,* amene ankaoneka ngati achule. Mauthengawo ankatuluka mʼkamwa mwa chinjoka,+ mʼkamwa mwa chilombo ndi mʼkamwa mwa mneneri wabodza. 14 Kwenikweni amenewa ndi mauthenga ouziridwa ndi ziwanda ndipo amachita zizindikiro.+ Mauthengawo akupita kwa mafumu a dziko lonse lapansi kumene kuli anthu, kuti awasonkhanitse pamodzi kunkhondo+ ya tsiku lalikulu la Mulungu Wamphamvuyonse.+

15 “Taona! Ndikubwera ngati wakuba.+ Wosangalala ndi amene akukhalabe maso+ ndiponso amene wavalabe malaya ake akunja, kuti asayende wosavala anthu nʼkuona maliseche ake.”+

16 Ndipo anawasonkhanitsa pamodzi, kumalo amene mʼChiheberi amatchulidwa kuti Aramagedo.*+

17 Mngelo wa 7 anakhuthulira mbale yake pampweya. Atatero, kunamveka mawu ofuula kuchokera mʼmalo opatulika,+ kuchokera kumpando wachifumu, akuti: “Zachitika!” 18 Ndiyeno kunachita mphezi, kunamveka mawu, kunagunda mabingu komanso kunachita chivomerezi chachikulu chimene sichinachitikepo kuyambira pamene munthu analengedwa padziko lapansi.+ Chivomerezicho chinali champhamvu kwambiri komanso chachikulu. 19 Mzinda waukulu+ unagawika zigawo zitatu ndipo mizinda ya mitundu ya anthu inagwa. Ndiyeno Mulungu anakumbukira Babulo Wamkulu,+ kuti amupatse kapu imene inali ndi vinyo wa mkwiyo wake waukulu.+ 20 Komanso chilumba chilichonse chinamira ndipo mapiri sanapezeke.+ 21 Kenako matalala aakulu, lililonse lolemera pafupifupi makilogalamu 20,* anagwera anthu kuchokera kumwamba.+ Anthuwo ananyoza Mulungu chifukwa cha mliri wa matalalawo,+ chifukwa mliriwo unali waukulu modabwitsa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena