Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 15
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la 1 Akorinto

      • Kuukitsidwa kwa Khristu (1-11)

      • Kuuka kwa akufa ndi maziko a chikhulupiriro (12-19)

      • Kuuka kwa Khristu kumatitsimikizira kuti akufa adzauka (20-34)

      • Thupi la mnofu ndiponso thupi lauzimu (35-49)

      • Thupi loti silingafe kapena kuwonongeka (50-57)

      • Kuchita zambiri pa ntchito ya Ambuye (58)

1 Akorinto 15:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 18:1, 11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, ptsa. 14-15

1 Akorinto 15:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, ptsa. 14-15

1 Akorinto 15:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 22:15; Yes 53:8, 12; Da 9:26; 1Pe 2:24

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 3

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, ptsa. 14-15

    2/15/1991, tsa. 5

1 Akorinto 15:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 53:9; Mt 27:59, 60
  • +Mt 28:7
  • +Yon 1:17; Lu 24:46
  • +Sl 16:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 3

1 Akorinto 15:5

Mawu a M'munsi

  • *

    Amatchedwanso Petulo.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 10:2; Lu 24:33, 34
  • +Yoh 20:26

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 3

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 4

    4/1/2010, tsa. 25

    7/1/1998, ptsa. 14-15

    1/15/1988, tsa. 30

    Tsanzirani, tsa. 202

    Mawu a Mulungu, ptsa. 82-86

1 Akorinto 15:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 28:16, 17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    “Wotsatira Wanga,” tsa. 97

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 3

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    7/2019, tsa. 14

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2015, ptsa. 26-27

    7/1/1998, ptsa. 14-16

    10/1/1995, tsa. 14

    5/1/1991, tsa. 8

    Yesu—Ndi Njira, tsa. 310

    Mawu a Mulungu, ptsa. 82-86

1 Akorinto 15:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 12:17
  • +Mac 1:3, 6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Muzikonda Anthu, lesson 8

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    1/2022, ptsa. 9-10

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 112

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 3

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2014, ptsa. 4-5

    7/1/1998, ptsa. 14-16

    Mawu a Mulungu, ptsa. 82-86

1 Akorinto 15:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 9:3-5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2022, tsa. 27

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 3

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2000, tsa. 29

    7/1/1998, ptsa. 14-16

    Mawu a Mulungu, ptsa. 82-86

1 Akorinto 15:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 8:3; Aga 1:13

1 Akorinto 15:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2013, ptsa. 23-24

    8/1/2000, tsa. 14

1 Akorinto 15:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 4:2; 17:31

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 5

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, ptsa. 14, 16-17

    8/15/1997, tsa. 12

    8/1/1993, tsa. 16

    9/15/1990, tsa. 25

1 Akorinto 15:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 4

1 Akorinto 15:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 4

    8/15/1997, tsa. 12

1 Akorinto 15:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 3:15
  • +Mac 2:24; 4:10; 13:30, 31

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 4

1 Akorinto 15:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 4:25; Ahe 7:25

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 4

    7/1/1998, ptsa. 16-17

1 Akorinto 15:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 7:59; 1Ak 15:14; 1Pe 1:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, ptsa. 5-6

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 4

    7/1/1998, ptsa. 16-17

1 Akorinto 15:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 4

    7/1/1998, ptsa. 16-17

1 Akorinto 15:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 26:23; Akl 1:18

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, ptsa. 5-6

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 7

    7/15/2007, tsa. 26

    7/15/2000, ptsa. 13-14

    7/1/1998, tsa. 17

    3/1/1998, tsa. 13

    1/1/1987, tsa. 25

1 Akorinto 15:21

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 3:17, 19
  • +Yoh 11:25

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 5

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 7

    7/1/1998, tsa. 17

1 Akorinto 15:22

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 5:12
  • +Aro 5:17; 6:23

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, ptsa. 5-6, 30

    Nsanja ya Olonda (Yogawira),

    No. 2 2017, tsatsa. 5-6

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 7

    7/1/1998, tsa. 17

    Kukambitsirana, tsa. 95

1 Akorinto 15:23

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Matanthauzo a Mawu Ena.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 1:5
  • +Mt 24:3; 1At 4:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 6

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2017, ptsa. 11-12

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2007, tsa. 26

    7/15/2000, ptsa. 13-14

    7/1/1998, ptsa. 17, 22-24

    10/1/1986, ptsa. 25-26

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 172-173

1 Akorinto 15:24

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 2:44

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 291, 300

    Lambirani Mulungu, tsa. 189

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/2000, tsa. 20

    7/1/1998, tsa. 21

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 182

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 180-182

1 Akorinto 15:25

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 110:1, 2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/1986, tsa. 25

1 Akorinto 15:26

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 20:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 30

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, ptsa. 6-7

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/2014, ptsa. 23-27

    9/15/2012, tsa. 11

    7/1/1998, ptsa. 21-22

    10/1/1986, tsa. 25

    Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, tsa. 237

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 291, 300

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 182

1 Akorinto 15:27

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 8:6; Aef 1:22
  • +Ahe 2:8
  • +1Pe 3:22

1 Akorinto 15:28

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 14:28
  • +1Ak 3:23

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Utumiki Komanso Moyo Wathu,

    4/2019, tsa. 6

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/2014, tsa. 27

    9/15/2012, ptsa. 11-12

    12/1/2007, tsa. 30

    7/1/1998, tsa. 22

    6/1/1994, ptsa. 30-31

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 180-189

1 Akorinto 15:29

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 6:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 14

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2008, tsa. 27

    10/1/2003, tsa. 29

    8/15/2000, tsa. 30

    7/15/2000, tsa. 17

    7/1/1998, ptsa. 17-18

    Kukambitsirana, ptsa. 366-367

1 Akorinto 15:30

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 8:36; 2Ak 11:23-27

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, ptsa. 17-18

1 Akorinto 15:31

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, tsa. 18

1 Akorinto 15:32

Mawu a M'munsi

  • *

    Mabaibulo ena amati, “mogwirizana ndi kuona kwa anthu.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 1:8
  • +Yes 22:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 163

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 9

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 3

    10/15/2007, tsa. 3

    6/15/2002, ptsa. 26-28

    7/15/2000, tsa. 18

    7/1/1998, tsa. 18

    11/1/1997, ptsa. 24-25

    8/15/1997, tsa. 12

    11/1/1996, tsa. 16

    9/15/1990, tsa. 25

    2/15/1989, tsa. 5

    6/15/1988, ptsa. 18-19

1 Akorinto 15:33

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “Musasocheretsedwe.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Miy 13:20; 1Ak 5:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    2/2023, ptsa. 17-18

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 48

    Galamukani!,

    No. 3 2019, tsa. 9

    9/8/2005, ptsa. 13-14

    8/8/2005, ptsa. 11-13

    3/8/1997, tsa. 24

    1/8/1994, ptsa. 16-17

    2/8/1990, tsa. 27

    Nsanja ya Olonda,

    8/15/2015, ptsa. 25-26

    7/15/2012, tsa. 15

    5/1/2007, ptsa. 15-16

    3/15/2006, tsa. 23

    7/15/2000, tsa. 18

    7/1/1998, tsa. 18

    11/1/1997, ptsa. 23-25

    7/15/1997, tsa. 18

    2/1/1994, tsa. 17

    8/1/1993, ptsa. 15-20

    8/15/1991, tsa. 29

    7/15/1991, ptsa. 23-24

    6/15/1988, ptsa. 18-19

    3/15/1987, tsa. 6

    Tsiku la Yehova, ptsa. 134-136

1 Akorinto 15:34

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, tsa. 18

    6/15/1988, ptsa. 18-19

1 Akorinto 15:35

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Yo 3:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, ptsa. 10-11

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2000, tsa. 18

    7/1/1998, tsa. 19

1 Akorinto 15:36

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, ptsa. 19-20

1 Akorinto 15:37

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 10

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, ptsa. 19-20

1 Akorinto 15:38

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 10

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, ptsa. 19-20

1 Akorinto 15:40

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 28:3; Lu 24:4
  • +Ahe 2:6, 7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, ptsa. 10-11

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2000, tsa. 18

    7/1/1998, tsa. 20

1 Akorinto 15:41

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 1:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, ptsa. 10-11

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, tsa. 20

    6/15/1993, tsa. 11

1 Akorinto 15:42

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 2:6, 7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 11

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2000, tsa. 18

    7/1/1998, tsa. 20

1 Akorinto 15:43

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Akl 3:4
  • +Chv 20:4

1 Akorinto 15:45

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 2:7
  • +Yoh 5:26; 1Ti 3:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Yandikirani, tsa. 145

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 11

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/2014, tsa. 26

    3/15/2000, tsa. 4

    2/15/1991, tsa. 14

    7/15/1990, tsa. 23

    8/15/1989, ptsa. 11-12, 13-14

    Galamukani!,

    5/8/2005, tsa. 16

    Mphunzitsi Waluso, ptsa. 192-193

    Kukambitsirana, tsa. 26

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 163-164, 169

1 Akorinto 15:47

Mawu a M'munsi

  • *

    Mʼchilankhulo choyambirira, “fumbi.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 2:7
  • +Yoh 3:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/1991, tsa. 14

    Kukambitsirana, tsa. 26

1 Akorinto 15:48

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Afi 3:20, 21

1 Akorinto 15:49

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 5:3
  • +Aro 8:29

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 11

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, tsa. 20

1 Akorinto 15:50

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 11

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2145

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/1993, tsa. 6

1 Akorinto 15:51

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1At 4:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 12

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, tsa. 17

    2/15/1995, tsa. 22

    1/15/1993, tsa. 6

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 173

1 Akorinto 15:52

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1At 4:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 12

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, tsa. 17

    2/15/1995, tsa. 22

    1/15/1993, tsa. 6

1 Akorinto 15:53

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 2:6, 7
  • +2Ak 5:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 25

    7/1/1998, tsa. 20

1 Akorinto 15:54

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “yathetsedwa.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 25:8; Chv 20:6

1 Akorinto 15:55

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ho 13:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2005, tsa. 29

    2/15/1995, tsa. 10

1 Akorinto 15:56

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 6:23
  • +Aro 3:20; 7:12, 13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2005, tsa. 29

    7/15/2000, tsa. 19

1 Akorinto 15:57

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 3:16; Mac 4:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, tsa. 24

1 Akorinto 15:58

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Akl 1:23; Ahe 3:14; 2Pe 3:17
  • +Aro 12:11
  • +2Mb 15:7; 1Ak 3:8; Chv 14:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 13

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    1/2017, ptsa. 9-10

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2003, tsa. 22

    7/15/2000, tsa. 19

    7/1/1998, tsa. 24

    7/1/1992, ptsa. 28-29

    10/15/1989, tsa. 20

    Utumiki wa Ufumu,

    6/2000, tsa. 1

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

1 Akor. 15:1Mac 18:1, 11
1 Akor. 15:3Sl 22:15; Yes 53:8, 12; Da 9:26; 1Pe 2:24
1 Akor. 15:4Yes 53:9; Mt 27:59, 60
1 Akor. 15:4Mt 28:7
1 Akor. 15:4Yon 1:17; Lu 24:46
1 Akor. 15:4Sl 16:10
1 Akor. 15:5Mt 10:2; Lu 24:33, 34
1 Akor. 15:5Yoh 20:26
1 Akor. 15:6Mt 28:16, 17
1 Akor. 15:7Mac 12:17
1 Akor. 15:7Mac 1:3, 6
1 Akor. 15:8Mac 9:3-5
1 Akor. 15:9Mac 8:3; Aga 1:13
1 Akor. 15:12Mac 4:2; 17:31
1 Akor. 15:15Mac 3:15
1 Akor. 15:15Mac 2:24; 4:10; 13:30, 31
1 Akor. 15:17Aro 4:25; Ahe 7:25
1 Akor. 15:18Mac 7:59; 1Ak 15:14; 1Pe 1:3
1 Akor. 15:20Mac 26:23; Akl 1:18
1 Akor. 15:21Ge 3:17, 19
1 Akor. 15:21Yoh 11:25
1 Akor. 15:22Aro 5:12
1 Akor. 15:22Aro 5:17; 6:23
1 Akor. 15:23Chv 1:5
1 Akor. 15:23Mt 24:3; 1At 4:16
1 Akor. 15:24Da 2:44
1 Akor. 15:25Sl 110:1, 2
1 Akor. 15:26Chv 20:14
1 Akor. 15:27Sl 8:6; Aef 1:22
1 Akor. 15:27Ahe 2:8
1 Akor. 15:271Pe 3:22
1 Akor. 15:28Yoh 14:28
1 Akor. 15:281Ak 3:23
1 Akor. 15:29Aro 6:4
1 Akor. 15:30Aro 8:36; 2Ak 11:23-27
1 Akor. 15:322Ak 1:8
1 Akor. 15:32Yes 22:13
1 Akor. 15:33Miy 13:20; 1Ak 5:6
1 Akor. 15:351Yo 3:2
1 Akor. 15:40Mt 28:3; Lu 24:4
1 Akor. 15:40Ahe 2:6, 7
1 Akor. 15:41Ge 1:16
1 Akor. 15:42Aro 2:6, 7
1 Akor. 15:43Akl 3:4
1 Akor. 15:43Chv 20:4
1 Akor. 15:45Ge 2:7
1 Akor. 15:45Yoh 5:26; 1Ti 3:16
1 Akor. 15:47Ge 2:7
1 Akor. 15:47Yoh 3:13
1 Akor. 15:48Afi 3:20, 21
1 Akor. 15:49Ge 5:3
1 Akor. 15:49Aro 8:29
1 Akor. 15:511At 4:17
1 Akor. 15:521At 4:16
1 Akor. 15:53Aro 2:6, 7
1 Akor. 15:532Ak 5:4
1 Akor. 15:54Yes 25:8; Chv 20:6
1 Akor. 15:55Ho 13:14
1 Akor. 15:56Aro 6:23
1 Akor. 15:56Aro 3:20; 7:12, 13
1 Akor. 15:57Yoh 3:16; Mac 4:12
1 Akor. 15:58Akl 1:23; Ahe 3:14; 2Pe 3:17
1 Akor. 15:58Aro 12:11
1 Akor. 15:582Mb 15:7; 1Ak 3:8; Chv 14:13
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
  • 23
  • 24
  • 25
  • 26
  • 27
  • 28
  • 29
  • 30
  • 31
  • 32
  • 33
  • 34
  • 35
  • 36
  • 37
  • 38
  • 39
  • 40
  • 41
  • 42
  • 43
  • 44
  • 45
  • 46
  • 47
  • 48
  • 49
  • 50
  • 51
  • 52
  • 53
  • 54
  • 55
  • 56
  • 57
  • 58
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
1 Akorinto 15:1-58

Kalata Yoyamba Yopita kwa Akorinto

15 Tsopano abale, ndikukukumbutsani za uthenga wabwino umene ndinaulalikira kwa inu,+ umenenso inuyo munaulandira ndiponso kuukhulupirira. 2 Mukupulumutsidwa ngati mwagwira mwamphamvu uthenga wabwino umene ndinaulalikirawo. Koma ngati simunaugwire mwamphamvu ndiye kuti kukhala kwanu okhulupirira kulibe phindu.

3 Pa zinthu zoyambirira zimene ndinakuphunzitsani, zomwenso ineyo ndinalandira, panali zonena kuti, Khristu anafera machimo athu, mogwirizana ndi Malemba.+ 4 Ndiponso kuti anaikidwa mʼmanda,+ kenako anaukitsidwa+ pa tsiku lachitatu,+ mogwirizana ndi Malemba.+ 5 Panalinso zoti anaonekera kwa Kefa,*+ kenako kwa atumwi 12 aja.+ 6 Ndiyeno anaonekeranso kwa abale oposa 500 pa nthawi imodzi,+ ndipo ambiri a iwo tidakali nawo, koma ena anagona mu imfa. 7 Atatero anaonekera kwa Yakobo,+ kenako kwa atumwi onse.+ 8 Koma pomaliza anaonekera kwa ine,+ ngati khanda lobadwa masiku osakwana.

9 Ineyo ndine wamngʼono kwambiri pa atumwi onse ndipo si ine woyenera kutchedwa mtumwi, chifukwa ndinazunza mpingo wa Mulungu.+ 10 Koma chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu, ndili mmene ndililimu. Ndipo kukoma mtima kwakukulu kumene anandisonyeza sikunapite pachabe, koma ndinagwira ntchito mwakhama kuposa atumwi ena onse. Komabe sindinachite zimenezi ndi mphamvu zanga zokha, koma chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu. 11 Kaya munaphunzitsidwa ndi ineyo kapena iwowo, uthenga umene tikulalikira ndi womwewo, umenenso munaukhulupirira.

12 Tsopano ngati timalalikira kuti Khristu anaukitsidwa,+ nʼchifukwa chiyani ena a inu akunena kuti akufa sadzaukitsidwa? 13 Chifukwa ngati akufa sadzauka, ndiye kuti Khristu nayenso sanaukitsidwe. 14 Komanso ngati Khristu sanaukitsidwe, kulalikira kwathu nʼkopanda phindu, ndipo chikhulupiriro chanu nʼchopandanso phindu. 15 Ndiponso, ndiye kuti ndife mboni zonama za Mulungu,+ chifukwa ngati akufa sadzaukadi, tapereka umboni wonamizira Mulungu kuti anaukitsa Khristu+ pamene sanamuukitse. 16 Chifukwa ngati akufa sadzauka, Khristunso sanaukitsidwe. 17 Ndipo ngati Khristu sanaukitsidwe, chikhulupiriro chanu nʼchopanda ntchito ndipo machimo anu sanakhululukidwe.+ 18 Ndiye kutinso otsatira a Khristu amene anagona mu imfa, zawo zinathera pomwepo.+ 19 Ngati chiyembekezo chathu mwa Khristu ndi cha moyo uno wokha, ndiye kuti ndife omvetsa chisoni kuposa anthu ena onse.

20 Komabe, Khristu anaukitsidwa nʼkukhala ngati chipatso choyambirira cha amene akugona mu imfa.+ 21 Popeza imfa inabwera kudzera mwa munthu mmodzi,+ kuuka kwa akufa kunabweranso kudzera mwa munthu mmodzi.+ 22 Monga zilili kuti anthu onse amafa chifukwa cha Adamu,+ anthu onse adzapatsidwanso moyo kudzera mwa Khristu.+ 23 Koma aliyense pa nthawi yoyenera: Choyamba Khristu, amene ndi chipatso choyambirira,+ kenako anthu a Khristu pa nthawi ya kukhalapo* kwake.+ 24 Ndiyeno pamapeto pa zonse, adzapereka Ufumu kwa Mulungu wake ndi Atate wake, atathetsa maboma onse, ulamuliro wonse ndi mphamvu zonse.+ 25 Chifukwa ayenera kukhala mfumu nʼkumalamulira mpaka Mulungu ataika adani onse pansi pa mapazi ake.+ 26 Imfa nayonso, yomwe ndi mdani womaliza, idzawonongedwa.+ 27 Mulungu “anaika zinthu zonse pansi pa mapazi ake.”+ Koma pamene akunena kuti ‘waika zinthu zonse pansi pake,’+ nʼzodziwikiratu kuti sakuphatikizapo Mulunguyo, amene anaika zinthu zonsezo pansi pa iye.+ 28 Koma zinthu zonse zikadzakhala pansi pake, Mwanayonso adzasonyeza kuti ali pansi pa ulamuliro wa Mulungu,+ kuti Mulungu akhale zinthu zonse kwa aliyense.+

29 Apo ayi, kodi amene akubatizidwa kuti akhale akufa adzatani?+ Ngati akufa sadzaukitsidwa, nʼchifukwa chiyani anthuwo akubatizidwa kuti akhale akufa? 30 Nʼchifukwa chiyaninso ifeyo tikuika moyo wathu pachiswe nthawi zonse?+ 31 Tsiku lililonse ndimakhala pa ngozi yoti ndikhoza kufa. Zimenezi nʼzoona ngati mmene zilili zoona kuti ndimakunyadirani chifukwa cha ubwenzi wanu ndi Khristu Yesu Ambuye wathu. 32 Ngati ndinamenyana ndi zilombo ku Efeso+ ngati mmene enanso anachitira,* ndinapindulapo chiyani? Ngati akufa sadzauka, “tiyeni tidye ndi kumwa chifukwa mawa tifa.”+ 33 Musapusitsidwe.* Kugwirizana ndi anthu oipa kumawononga makhalidwe abwino.+ 34 Yambani kuganiza mwanzeru nʼkumachita zoyenera ndipo musamachite tchimo. Ena a inu sadziwa Mulungu. Ndikulankhula zimenezi kuti ndikuchititseni manyazi.

35 Komabe, wina anganene kuti: “Kodi akufa adzaukitsidwa bwanji? Nanga adzauka ndi thupi lotani?”+ 36 Wosaganiza bwino iwe! Ukadzala chinthu sichikhala ndi moyo pokhapokha chitafa kaye. 37 Ndipo ukamadzala, sudzala mmera wokula kale, koma mbewu chabe, kaya ya tirigu kapena ina iliyonse. 38 Koma Mulungu amaikulitsa mogwirizana ndi kufuna kwake, ndipo mbewu iliyonse ikamakula sifanana ndi inzake. 39 Zinthu zonse zimene zimakhala ndi mnofu sizikhala zofanana. Anthu, nyama, mbalame ndiponso nsomba zili ndi mnofu, koma chilichonse nʼchosiyana ndi chinzake. 40 Palinso matupi akumwamba+ ndiponso matupi apadziko lapansi,+ koma ulemerero wa matupi akumwamba ndi wosiyana ndi ulemerero wa matupi apadziko lapansi. 41 Ulemerero wa dzuwa ndi wosiyana ndi ulemerero wa mwezi+ kapenanso wa nyenyezi. Ndipotu ulemerero wa nyenyezi ina, umasiyananso ndi wa nyenyezi ina.

42 Ndi mmenenso zilili ndi kuuka. Thupi limene limakwiriridwa limakhala loti lingawonongeke, koma limene limaukitsidwa limakhala loti silingawonongeke.+ 43 Limakwiriridwa lili lonyozeka, koma limaukitsidwa lili laulemerero.+ Limakwiriridwa lili lofooka, koma limaukitsidwa lili lamphamvu.+ 44 Limakwiriridwa lili thupi la mnofu, koma limaukitsidwa thupi lauzimu. Ngati pali thupi la mnofu, palinso lauzimu. 45 Paja Malemba amati: “Adamu, yemwe anali munthu woyambirira, anakhala munthu wamoyo.”+ Adamu womalizira anakhala mzimu wopatsa moyo.+ 46 Komabe, amene anayamba kubwera si munthu wauzimuyo. Munthu wokhala ndi mnofu ndi amene anayamba kubwera kenako munthu wauzimu. 47 Munthu woyambayo anachokera padziko lapansi ndipo anapangidwa ndi dothi.*+ Wachiwiriyo anachokera kumwamba.+ 48 Anthu opangidwa ndi dothi ali ngati munthu woyambayo amene anapangidwa ndi dothi. Ndipo akumwamba ali ngati wochokera kumwambayo.+ 49 Monga zilili kuti panopa tikufanana ndi wopangidwa ndi dothi uja,+ tidzafanananso ndi wakumwambayo.+

50 Koma abale, dziwani kuti mnofu ndi magazi sizingalowe mu Ufumu wa Mulungu. Komanso chinthu chimene chingawonongeke sichingalandire kusawonongeka. 51 Tamverani, ndikuuzeni chinsinsi chopatulika: Sikuti tonse tidzagona mu imfa, koma tonse tidzasintha,+ 52 mʼkanthawi kochepa, mʼkuphethira kwa diso, pa kulira kwa lipenga lomaliza. Chifukwa lipenga lidzalira,+ kenako akufa adzaukitsidwa ndi matupi oti sangawonongeke ndipo tidzasintha. 53 Chifukwa matupi oti akhoza kuwonongekawa adzasintha nʼkukhala oti sangawonongeke.+ Ndipo matupi oti angafewa adzasintha nʼkukhala oti sangafe.+ 54 Koma matupi oti akhoza kuwonongekawa akadzakhala oti sangawonongeke komanso matupi oti angafewa akadzasintha nʼkukhala oti sangafe, zimene Malemba amanena zidzakwaniritsidwa, zakuti: “Imfa yamezedwa* kwamuyaya.”+ 55 “Iwe Imfa, kupambana kwako kuli kuti? Iwe Imfa, amene umabweretsa ululu woopsa, kodi mphamvu yako ili kuti?”+ 56 Mphamvu imene imabweretsa imfa ndi uchimo,+ koma Chilamulo nʼchimene chimasonyeza mphamvu ya uchimo.+ 57 Koma tikuthokoza Mulungu chifukwa amatithandiza kuti tipambane kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu.+

58 Choncho abale anga okondedwa, khalani olimba+ ndiponso osasunthika. Nthawi zonse muzikhala ndi zochita zambiri+ pa ntchito ya Ambuye, podziwa kuti zonse zimene mukuchita pa ntchito ya Ambuye sizidzapita pachabe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena